Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 5:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Limodzi la magawo ace atatu utenthe ndi moto pakati pa mudzi pakutha masiku a kuzingidwa mudzi, nutenge gawo lina ndi kukwapula-kwapula ndi lupanga pozungulira pace, nuwaze kumphepo gawo lotsala; pakuti ndidzasolola lupanga lakuwatsata.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 5

Onani Ezekieli 5:2 nkhani