Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 5:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, udzitengere mpeni wakuthwa, ndiwo lumo la wometa, udzitengere ndi kulipititsa pamutu pako ndi pa ndebvu zako; nudzitengere muyeso kuyesa nao, ndi kugawa tsitsilo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 5

Onani Ezekieli 5:1 nkhani