Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 5:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Limodzi la magawo atatu la iwe lidzafa ndi mliri, nilidzatha ndi njala pakati pa iwe; ndi limodzi lidzagwa ndi lupanga pozinga pako; ndi limodzi ndidzalibalalikitsa ku mphepo zonse, ndi kuwasololera lupanga lakuwatsata.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 5

Onani Ezekieli 5:12 nkhani