Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 47:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzatero kuti zamoyo zonse zocuruka zidzakhala ndi moyo kuti konse mtsinjewo ufikako, ndi nsomba zidzacuruka kwambiri; pakuti madzi awa anafikako, nakonzeka madzi a m'nyanja; ndipo kuli konse mtsinje ufikako ziri zonse zidzakhala ndi moyo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 47

Onani Ezekieli 47:9 nkhani