Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 47:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anati kwa ine, Madzi awa aturukira ku dera la kum'mawa, natsikira kucidikha, nayenda kunyanja; atathira kunyanja akonzeka madzi ace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 47

Onani Ezekieli 47:8 nkhani