Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 47:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Poturuka munthuyu kumka kum'mawa ndi cingwe coyesera m'dzanja lace, anayesa mikono cikwi cimodzi, nandipititsa pamadzi, madzi oyesa m'kakolo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 47

Onani Ezekieli 47:3 nkhani