Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 46:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kalonga azilowera njira ya ku khonde la cipataco, kunja kwace, naime ku nsanamira ya cipata; ndipo ansembe akonze nsembe yace yopsereza, ndi nsembe zace zoyamika, nalambire iye ku ciundo ca cipata; atatero aturuke; koma pacipata pasatsekedwe mpaka madzulo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 46

Onani Ezekieli 46:2 nkhani