Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 46:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kalonga akapereka copereka caufulu nsembe yopsereza, kapena nsembe zoyamika kwa Yehova, amtsegulire pa cipata coloza kum'mawa; ndipo azipereka nsembe yace yopsereza, ndi nsembe zace zoyamika, monga umo amacitira tsiku la Sabata; atatero aturuke; ndipo ataturuka, wina atseke pacipata.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 46

Onani Ezekieli 46:12 nkhani