Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 45:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Efa ndi bati zikhale za muyeso umodzi, bati liyese limodzi la magawo khumi la homeri, efa lomwe liyese limodzi la magawo khumi la homeri; muyeso wao uyesedwa monga mwa homeri.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 45

Onani Ezekieli 45:11 nkhani