Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 44:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, samalira bwino, nupenye ndi maso ako, numve m'makutu mwako zonse ndidzanena nawe, kunena za malemba onse a nyumba ya Yehova, ndi malamulo ace onse; nusamalire bwino malowedwe a nyumbayi, ndi maturukidwe ace onse a malo opatulika.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 44

Onani Ezekieli 44:5 nkhani