Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 44:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atatero anamuka nane njira ya cipata ca kumpoto kukhomo kwa kacisi, ndipo ndinapenya, taonani, ulemerero wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehova; pamenepo ndinagwa nkhope pansi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 44

Onani Ezekieli 44:4 nkhani