Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 44:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakakhala mlandu, aimeko kuweruza; auweruze monga mwa maweruzo anga, ndipo azisunga malamulo anga, ndi malemba anga, pa madyerero anga onse oikika; napatulikitse masabata anga.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 44

Onani Ezekieli 44:24 nkhani