Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 44:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzatero, polowa iwo ku zipata za bwalo lam'kati abvale zobvala zabafuta; koma zaubweya asazibvale ponditumikira Ine m'zipata za bwalo la m'kati, ndi m'kacisi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 44

Onani Ezekieli 44:17 nkhani