Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 42:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atalowa ansembe asaturukenso m'malo opatulika kumka ku bwalo lakunja, koma komweko aziika zobvala zao zimene atumikira nazo; pakuti ziri zopatulika; ndipo abvale zobvala zina, nayandikire zinthu wamba za anthu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 42

Onani Ezekieli 42:14 nkhani