Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 41:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali mazenera a made okhazikika, ndi akanjedza cakuno ndi cauko, kumbali zace za khonde; momwemonso pa zipinda za m'mphepete mwa nyumba, ndi pa matabwa ocindikira.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 41

Onani Ezekieli 41:26 nkhani