Ndipo iwe ugonere pansi mbali yako ya kumanzere, nuikepo mphulupulu ya nyumba ya Israyeli; monga mwa kuwerenga kwa masiku amene udzagonapo udzasenza mphulupulu yao.