Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 4:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanenanso nane, Wobadwa ndi munthu iwe, taona, ndidzatyola mcirikizo, ndiwo cakudya, m'Yerusalemu; ndipo adzadya cakudyaco monga mwa muyeso, ndi mosamalira, nadzamwa madzi monga mwa muyeso, ndi kudabwa;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 4

Onani Ezekieli 4:16 nkhani