Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 37:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'mwemo ndinanenera monga anandiuza, ndipo ponenera ine panali phokoso; ndipo taonani, panali gobede gobede, ndi mafupa anasendererana, pfupa kutsata pfupa linzace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 37

Onani Ezekieli 37:7 nkhani