Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 37:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzakhala m'dziko ndinalipereka kwa Yakobo mtumiki wanga, limene anakhalamo makolo anu, ndipo adzakhala m'mwemo iwo, ndi ana ao, ndi zidzukulu zao kosatha; ndi Davide mtumiki wanga adzakhala mtsogoleri wao kosatha.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 37

Onani Ezekieli 37:25 nkhani