Cifukwa cace, nenera, nunene nao, Atero Ambuye Yehova, Taonani anthu anga, ndidzatsegula kumanda kwanu, ndi kukweza inu muturuke m'manda mwanu, ndipo ndidzakulowetsani m'dziko la Israyeli.