Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 34:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo mau a Yehova anandidzera, akuti,

2. Wobadwa ndi munthu iwe, Nenera motsutsa abusa a Israyeli; nenera, nuti nao abusawo, Atero Ambuye Yehova, Tsoka abusa a Israyeli odzidyetsa okha; kodi abusa sayenera kudyetsa nkhosa?

3. Mukudya mafuta, mubvala ubweya, mukupha zonenepa; koma simudyetsa nkhosa.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 34