Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 34:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wobadwa ndi munthu iwe, Nenera motsutsa abusa a Israyeli; nenera, nuti nao abusawo, Atero Ambuye Yehova, Tsoka abusa a Israyeli odzidyetsa okha; kodi abusa sayenera kudyetsa nkhosa?

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 34

Onani Ezekieli 34:2 nkhani