Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 33:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akudzera monga amadzera anthu, nakhala pansi pamaso pako ngati anthu anga, namva mau ako, koma osawacita; pakuti pakamwa pao anena mwacikondi, koma mtima wao utsata phindu lao.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 33

Onani Ezekieli 33:31 nkhani