Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 32:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Elamu ali komwe ndi gulu lace lonse lozinga manda ace; ophedwa onsewo, adagwa ndi lupanga; amene anatsikira osadulidwa kunsi kwace kwa dziko, amene anaopsetsa m'dziko la amoyo, nasenza manyazi ao, pamodzi ndi iwo akutsikira kudzenje.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 32

Onani Ezekieli 32:24 nkhani