Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 32:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakusanduliza Ine dziko la Aigupto likhale lopasuka ndi labwinja, dziko losowa zodzaza zace, pakukantha Ine onse okhala m'mwemo, pamenepo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 32

Onani Ezekieli 32:15 nkhani