Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 3:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pamene ndilankhula nawe ndidzatsegula pakamwa pako, nudzanena nao, Atero Yehova Mulungu. Wakumvera amvere, wasafuna kumvera akhale; pakuti iwo ndiwo nyumba yopanduka.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3

Onani Ezekieli 3:27 nkhani