Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 3:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo ananena nane, Wobadwa ndi munthu iwe, Idya cimene wacipeza; idya mpukutu uwu, numuke ndi kunena ndi nyumba ya Israyeli.

2. Pamenepo ndinatsegula pakamwa panga ndipo anandidyetsa mpukutuwo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3