Ndipo ananena nane, Wobadwa ndi munthu iwe, Idya cimene wacipeza; idya mpukutu uwu, numuke ndi kunena ndi nyumba ya Israyeli.