Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 29:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace atero Ambuye Yehova, Taona, ndidzapereka dziko la Aigupto kwa Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo; ndipo adzacoka nao aunyinji ace, nadzafunkha ndi kulanda zace, ndizo mphotho ya khamu lace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 29

Onani Ezekieli 29:19 nkhani