Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 28:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. taona, ndiwe wanzeru woposa Danieli, palibe cinsinsi angakubisire;

4. mwa nzeru zako ndi luntha lako wadzionerera cuma, wadzionereranso golidi ndi siliva mwa cuma cako;

5. mwa nzeru zako zazikuru ndi kugulana malonda kwako wacurukitsa cuma cako, ndi mtima wako wadzikuza cifukwa ca cuma cako;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 28