Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 28:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wobadwa ndi munthu iwe, uziti kwa kalonga wa Turo, Atero Ambuye Yehova, Popeza mtima wako wadzikweza, nuti, Ine ndine mulungu, ndikhala pa mpando wa Mulungu pakati pa nyanja, ungakhale uli munthu, wosati Mulungu, ungakhale waika mtima wako ngati mtima wa Mulungu,

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 28

Onani Ezekieli 28:2 nkhani