Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 28:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

uziti, Atero Ambuye Yehova, Taona, nditsutsana nawe Zidoni, ndipo ndidzalemekezedwa pakati pako; ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova pakucita Ine maweruzo mwa uwu, ndi kuzindikiridwa Woyera mwa uwu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 28

Onani Ezekieli 28:22 nkhani