Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 27:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu a Ativadi pamodzi ndi ankhondo ako anali pa malinga ako pozungulira, ndi Agamadi anali mu nsanja zako; anapacika zikopa zao pa makoma ako pozungulira, anakwaniritsa kukoma kwako.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 27

Onani Ezekieli 27:11 nkhani