Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 21:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, nenera, nuziti, Atero Ambuye Yehova za ana a Amoni, ndi za citonzo cao; nuziti, Lupanga, lupanga lasololedwa, latuulidwa, kuti likaphe, kuti liononge, likhale lonyezimira.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 21

Onani Ezekieli 21:28 nkhani