Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 20:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anapandukira Ine, osafuna kundimvera Ine, sanataya yense zonyansa pamaso pace, sanaleka mafano a Aigupto; pamenepo ndidati ndiwatsanulire ukali wanga, kuwakwaniritsira mkwiyo wanga m'dziko la Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:8 nkhani