Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 20:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova, pakukulowetsani Ine m'dzil ko la Israyeli, m'dzikoli ndinalikwezera dzanja langa kulipereka kwa makolo anu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:42 nkhani