Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 2:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwe, wobadwa ndi munthu iwe, usawaopa, kapena kuopa mau ao; ingakhale mitungwi ndi minga ikhala ndi iwe, nukhala pakati pa zinkhanira, usaopa mau ao kapena kuopsedwa ndi nkhope zao; pakuti ndiwo nyumba yopanduka.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 2

Onani Ezekieli 2:6 nkhani