Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 13:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'mwemo ndidzagumula linga munalimata ndi dothi losapondeka, ndi kuligwetsa pansi; kuti maziko ace agadabuke, ndipo lidzagwa; ndi inu mudzathedwa pakati pace; ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 13

Onani Ezekieli 13:14 nkhani