Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 1:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinapenya ngati citsulo cakupsa, ngati maonekedwe ace a moto m'kati mwace pozungulira pace, kuyambira maonekedwe a m'cuuno mwace ndi kumwamba kwace; ndipo kuyambira maonekedwe a m'cuuno mwace ndi kunsi kwace ndinaona ngati maonekedwe ace a moto; ndi kunyezimira kudamzinga.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 1

Onani Ezekieli 1:27 nkhani