Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 8:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi pa tsiku lacinai siliva ndi golidi ndi zipangizo zinayesedwa m'nyumba ya Mulungu wathu, m'dzanja la Meremoti mwana wa Uliya wansembe, ndi pamodzi naye Eleazara mwana wa Pinehasi, ndi pamodzi nao Yozabadi mwana wa Yesuwa, ndi Nowadia mwana wa Binui, Alevi;

Werengani mutu wathunthu Ezara 8

Onani Ezara 8:33 nkhani