Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 7:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

m'mwemo uzifulumira kugula ndi ndalama iyi ng'ombe, nkhosa zamphongo, ana a nkhosa, pamodzi ndi nsembe zao zaufa, ndi nsembe zao zothira; ndi kuzipereka pa guwa la nsembe la nyumba ya Mulungu wanu yokhala ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu Ezara 7

Onani Ezara 7:17 nkhani