Malemba a kalatayo mfumu Aritasasta anampatsa Ezara wansembe mlembi, ndiye mlembi wa mau a malamulo a Yehova, ndi malemba ace kwa Israyeli, ndi awa: