Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 6:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zosowa zao, ana a ng'ombe, ndi nkhosa zamphongo, ndi ana a nkhosa, zikhale nsembe zopsereza za Mulungu wa Kumwamba; tirigu, mcere, vinyo, mafuta, monga umo adzanena ansembe ali ku Yerusalemu, ziperekedwe kwa iwo tsiku ndi tsiku, zisasoweke;

Werengani mutu wathunthu Ezara 6

Onani Ezara 6:9 nkhani