Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 6:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndilamuliranso za ici muzicitira akuru awa a Ayuda, kuti amange nyumba iyi ya Mulungu, ndiko kuti mutengeko cuma ca mfumu, ndico msonkho wa tsidya la mtsinje, nimupereke zolipira kwa anthu awa msanga, angawacedwetse.

Werengani mutu wathunthu Ezara 6

Onani Ezara 6:8 nkhani