Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 6:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ansembe ndi Alevi anadziyeretsa pamodzi, anayera onsewo, naphera Paskha cifukwa ca ana onse a ndende, ndi abale ao ansembe, ndi iwo okha.

Werengani mutu wathunthu Ezara 6

Onani Ezara 6:20 nkhani