Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 4:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

anayandikira kwa Zerubabele, ndi kwa akulu a nyumba za makolo, nanena nao, Timange pamodzi nanu; pakuti timfuna Mulungu wanu monga inu, ndipo timamphera nsembe ciyambire masiku a Ezaradoni mfumu ya Asuri, amene anatikweretsa kuno.

Werengani mutu wathunthu Ezara 4

Onani Ezara 4:2 nkhani