Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 3:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Utakhala tsono mwezi wacisanu ndi ciwiri, ana a Israyeli ali m'midzimo, anthuwo anasonkhana ngati munthu mmodzi ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu Ezara 3

Onani Ezara 3:1 nkhani