Ndipo ansembe, ndi Alevi, ndi anthu ena, ndi oyimbira, ndi odikira, ndi Anetini, anakhala m'midzi mwao, ndi Aisrayeli onse m'midzi mwao.