Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 10:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anasonkhana ku Yerusalemu amuna onse a Yuda ndi Benjamini asanapite masiku atatu, ndiwo mwezi wacisanu ndi cinai, tsiku la makumi awiri a mwezi; nakhala pansi anthu onse m'khwalala pakhomo pa nyumba ya Mulungu, alikunjenjemera cifukwa ca mlandu uwu, ndi cifukwa ca mvulayi.

Werengani mutu wathunthu Ezara 10

Onani Ezara 10:9 nkhani