Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 10:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tsono, ululani kwa Yehova Mulungu wa makolo anu, nimucite comkondweretsa; mudzilekanitse ndi mitundu ya anthu a m'dzikomo, ndi kwa akazi acilendo.

Werengani mutu wathunthu Ezara 10

Onani Ezara 10:11 nkhani